Ekisodo 23:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Muzichita zonse zimene ndakuuzanizi mosamala,+ ndipo musatchule mayina a milungu ina. Asamveke pakamwa panu.+
13 Muzichita zonse zimene ndakuuzanizi mosamala,+ ndipo musatchule mayina a milungu ina. Asamveke pakamwa panu.+