-
Ekisodo 23:18Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
18 Mukamapereka magazi a nsembe yanga musawapereke limodzi ndi chilichonse chokhala ndi zofufumitsa. Ndipo nsembe za mafuta zimene mwapereka pazikondwerero zanga zisamagone mpaka mʼmawa.
-