Ekisodo 23:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Muzimumvera ndi kuchita zimene wanena. Musamupandukire, chifukwa sadzakukhululukirani zolakwa zanu,+ popeza dzina langa lili mwa iye. Ekisodo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 23:21 Nsanja ya Olonda,12/15/2010, tsa. 69/15/2010, tsa. 213/15/2004, tsa. 27
21 Muzimumvera ndi kuchita zimene wanena. Musamupandukire, chifukwa sadzakukhululukirani zolakwa zanu,+ popeza dzina langa lili mwa iye.