Ekisodo 23:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Sindidzawathamangitsa pamaso panu mʼchaka chimodzi, kuti dzikolo lisakhale bwinja ndiponso kuti zilombo zakutchire zisachuluke nʼkukuvutitsani.+
29 Sindidzawathamangitsa pamaso panu mʼchaka chimodzi, kuti dzikolo lisakhale bwinja ndiponso kuti zilombo zakutchire zisachuluke nʼkukuvutitsani.+