Ekisodo 25:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Kenako mulikute ndi golide woyenga bwino.+ Mkati ndi kunja komwe mulikute ndi golide, ndipo mupange mkombero wagolide kuzungulira likasalo.+
11 Kenako mulikute ndi golide woyenga bwino.+ Mkati ndi kunja komwe mulikute ndi golide, ndipo mupange mkombero wagolide kuzungulira likasalo.+