Ekisodo 25:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Kenako mupange choikapo nyale+ chagolide woyenga bwino. Choikapo nyalecho chikhale chinthu chimodzi chosula ndipo chikhale ndi tsinde, thunthu, nthambi, timasamba tamʼmunsi mwa duwa, mphindi ndi maluwa.+
31 Kenako mupange choikapo nyale+ chagolide woyenga bwino. Choikapo nyalecho chikhale chinthu chimodzi chosula ndipo chikhale ndi tsinde, thunthu, nthambi, timasamba tamʼmunsi mwa duwa, mphindi ndi maluwa.+