-
Ekisodo 26:4Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
4 Kumapeto kwa nsalu imodzi yaikulu, upange zingwe zopota zabuluu zokolekamo ngowe. Uchitenso chimodzimodzi kumapeto kwa nsalu inayo, pamalo amene nsalu ziwirizi zidzalumikizane.
-