-
Ekisodo 26:10Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
10 Uike zingwe zopota 50 zokolekamo ngowe mʼmphepete mwa nsalu yakumapeto kwenikweni kwa nsalu za chihema zolumikizanazo. Uikenso zingwe zopota 50 zokolekamo ngowe mʼmphepete mwa nsalu zina zolumikizana, pomwe magulu awiri a nsalu zomwe zalumikizanazo adzakumane.
-