-
Ekisodo 26:11Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
11 Upange ngowe 50 zakopa nʼkuzilowetsa mʼzingwe zopota zokolekamo ngowezo, nʼkulumikiza nsaluzo kuti zikhale chinsalu chimodzi chopangira chihema.
-