-
Ekisodo 26:13Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
13 Ndipo kumbali iliyonse mulitali mwa chinsalucho, mutsala nsalu yokwana masentimita 45. Nsalu yotsalayo izilendewera mpaka mʼmunsi kuti iphimbe chihemacho.
-