Ekisodo 26:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Upange zitsulo 40 zasiliva zokhazikapo mafelemu+ 20 aja. Zitsulo ziwiri zikhale pansi pa felemu lililonse kuti mulowe zolumikizira ziwiri.+
19 Upange zitsulo 40 zasiliva zokhazikapo mafelemu+ 20 aja. Zitsulo ziwiri zikhale pansi pa felemu lililonse kuti mulowe zolumikizira ziwiri.+