Ekisodo 26:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Upange chihemacho motsatira pulani yake imene ndakuonetsa mʼphiri.+