Ekisodo 27:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Upange bokosi lamatabwa losatseka pansi. Lipangidwe mogwirizana ndi mmene ndakusonyezera mʼphiri.+