-
Ekisodo 27:12Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
12 Mulifupi mwa bwalolo, kumbali yakumadzulo, mpanda wa nsaluwo kutalika kwake ukhale mamita 23, ndipo ukhale ndi zipilala 10 ndi zitsulo 10 zokhazikapo zipilalazo.
-