Ekisodo 27:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Kudzanja lamanja la geti la bwalolo, mpanda wa nsaluwo ukhale mamita 7 kutalika kwake. Kukhale zipilala zitatu ndi zitsulo zitatu zokhazikapo zipilalazo.+
14 Kudzanja lamanja la geti la bwalolo, mpanda wa nsaluwo ukhale mamita 7 kutalika kwake. Kukhale zipilala zitatu ndi zitsulo zitatu zokhazikapo zipilalazo.+