-
Ekisodo 27:15Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
15 Ndipo kudzanja lamanzere la geti la bwalolo mpanda wa nsaluwo ukhale mamita 7. Kukhale zipilala zitatu ndi zitsulo zitatu zokhazikapo zipilalazo.
-