18 Bwalolo mulitali mwake likhale mamita 45,+ mulifupi mwake mamita 23, ndipo kutalika kwake kuchoka pansi mpaka mʼmwamba kukhale mamita atatu. Nsalu zake zikhale za ulusi wopota wabwino kwambiri, ndipo zitsulo zake zokhazikapo zipilala zikhale zakopa.