Ekisodo 28:36 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 Upangenso kachitsulo konyezimira kagolide woyenga bwino ndipo ulembepo mochita kugoba ngati mmene amagobera chidindo, mawu akuti: ‘Yehova ndi Woyera.’+
36 Upangenso kachitsulo konyezimira kagolide woyenga bwino ndipo ulembepo mochita kugoba ngati mmene amagobera chidindo, mawu akuti: ‘Yehova ndi Woyera.’+