Ekisodo 29:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Kenako utenge zovala+ zija nʼkuveka Aroni. Umuveke mkanjo ndi malaya odula manja a mkati mwa efodi. Umuvekenso efodi ndi chovala pachifuwa komanso umumange lamba* woluka wa efodi mʼchiuno mwake.+
5 Kenako utenge zovala+ zija nʼkuveka Aroni. Umuveke mkanjo ndi malaya odula manja a mkati mwa efodi. Umuvekenso efodi ndi chovala pachifuwa komanso umumange lamba* woluka wa efodi mʼchiuno mwake.+