Ekisodo 29:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Umuveke nduwira pamutu pake ndipo panduwirapo uikepo chizindikiro chopatulika cha kudzipereka.+