Ekisodo 29:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Aroni ndi ana akewo uwamange malamba pamimba. Ana akewo uwakulunge mipango kumutu kwawo ndipo adzakhala ansembe.+ Limeneli ndi lamulo langa mpaka kalekale. Uchite zimenezi kuti uike Aroni ndi ana ake kuti akhale ansembe.*+
9 Aroni ndi ana akewo uwamange malamba pamimba. Ana akewo uwakulunge mipango kumutu kwawo ndipo adzakhala ansembe.+ Limeneli ndi lamulo langa mpaka kalekale. Uchite zimenezi kuti uike Aroni ndi ana ake kuti akhale ansembe.*+