Ekisodo 29:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Kenako utenge mafuta onse+ okuta matumbo, mafuta apachiwindi, impso ziwiri ndi mafuta ake nʼkuzitentha kuti paguwa lansembe pakhale utsi.+
13 Kenako utenge mafuta onse+ okuta matumbo, mafuta apachiwindi, impso ziwiri ndi mafuta ake nʼkuzitentha kuti paguwa lansembe pakhale utsi.+