Ekisodo 29:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Ndiyeno pankhosayo utengepo mafuta ndi mchira wa mafuta ndi mafuta okuta matumbo, mafuta apachiwindi, impso ziwiri ndi mafuta ake+ ndi mwendo wakumbuyo wakumanja, chifukwa nkhosayo ndi yowaikira kuti akhale ansembe.+
22 Ndiyeno pankhosayo utengepo mafuta ndi mchira wa mafuta ndi mafuta okuta matumbo, mafuta apachiwindi, impso ziwiri ndi mafuta ake+ ndi mwendo wakumbuyo wakumanja, chifukwa nkhosayo ndi yowaikira kuti akhale ansembe.+