Ekisodo 29:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Kenako uzitenge mʼmanja mwawo nʼkuziwotcha paguwa lansembe pamwamba pa nsembe yopsereza, kuti zikhale kafungo kosangalatsa* kwa Yehova. Imeneyi ndi nsembe yowotcha pamoto yoperekedwa kwa Yehova.
25 Kenako uzitenge mʼmanja mwawo nʼkuziwotcha paguwa lansembe pamwamba pa nsembe yopsereza, kuti zikhale kafungo kosangalatsa* kwa Yehova. Imeneyi ndi nsembe yowotcha pamoto yoperekedwa kwa Yehova.