Ekisodo 29:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Wansembe amene adzalowe mʼmalo mwake kuchokera pakati pa ana ake, amene adzalowe mʼchihema chokumanako kukatumikira mʼmalo oyera, azidzavala zovalazo kwa masiku 7.+
30 Wansembe amene adzalowe mʼmalo mwake kuchokera pakati pa ana ake, amene adzalowe mʼchihema chokumanako kukatumikira mʼmalo oyera, azidzavala zovalazo kwa masiku 7.+