Ekisodo 29:42 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 42 Mʼmibadwo yanu yonse, muzipereka nsembe yopsereza imeneyi nthawi zonse pakhomo la chihema chokumanako pamaso pa Yehova, kumene ndidzaonekera kwa inu kuti ndilankhule nanu.+
42 Mʼmibadwo yanu yonse, muzipereka nsembe yopsereza imeneyi nthawi zonse pakhomo la chihema chokumanako pamaso pa Yehova, kumene ndidzaonekera kwa inu kuti ndilankhule nanu.+