Ekisodo 30:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Uuze Aisiraeli kuti, ‘Mafuta awa akhale mafuta anga ogwiritsa ntchito pa kudzoza kopatulika mʼmibadwo yanu yonse.+
31 Uuze Aisiraeli kuti, ‘Mafuta awa akhale mafuta anga ogwiritsa ntchito pa kudzoza kopatulika mʼmibadwo yanu yonse.+