-
Ekisodo 32:5Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
5 Aroni ataona zimenezi, anamanga guwa lansembe patsogolo pa fanolo. Kenako iye anafuula kuti: “Mawa kuli chikondwerero cha Yehova.”
-