Ekisodo 32:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Ndiyeno Yehova anauza Mose kuti: “Pita, tsika, chifukwa anthu ako amene unawatsogolera potuluka mʼdziko la Iguputo aja achita zinthu zoipa.+ Ekisodo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 32:7 Mungakhale Ndi Moyo Mpaka Kalekale, lesson 44
7 Ndiyeno Yehova anauza Mose kuti: “Pita, tsika, chifukwa anthu ako amene unawatsogolera potuluka mʼdziko la Iguputo aja achita zinthu zoipa.+