-
Ekisodo 32:18Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
18 Koma Mose anati:
“Limeneli si phokoso la nyimbo ya kupambana,
Komanso si phokoso la anthu amene akulira chifukwa chogonjetsedwa;
Ndikumva ngati ndi kuimba kwa mtundu wina.”
-