Ekisodo 32:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Choncho anandiuza kuti, ‘Tipangire mulungu woti atitsogolere, chifukwa sitikudziwa zimene zachitikira Mose, amene ankatitsogolera pochoka ku Iguputo.’+
23 Choncho anandiuza kuti, ‘Tipangire mulungu woti atitsogolere, chifukwa sitikudziwa zimene zachitikira Mose, amene ankatitsogolera pochoka ku Iguputo.’+