-
Ekisodo 32:24Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
24 Ndiye ndinawauza kuti, ‘Aliyense amene wavala chinthu chagolide avule nʼkundipatsa.’ Kenako golideyo ndinamuponya pamoto nʼkukhala mwana wa ngʼombeyu.”
-