33 Yehova anapitiriza kulankhula ndi Mose kuti: “Nyamuka, uchoke pano limodzi ndi anthu amene unawatsogolera potuluka mʼdziko la Iguputo. Mupite kudziko limene ndinalumbira kwa Abulahamu, Isaki ndi Yakobo kuti, ‘Ndidzapereka dziko ili kwa mbadwa zako.’+