Ekisodo 34:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Koma usakwere mʼphirimo ndi wina aliyense, ndipo musapezeke wina aliyense mmenemo. Ngakhale nkhosa kapena ngʼombe zisadye mʼmunsi mwa phirilo.”+
3 Koma usakwere mʼphirimo ndi wina aliyense, ndipo musapezeke wina aliyense mmenemo. Ngakhale nkhosa kapena ngʼombe zisadye mʼmunsi mwa phirilo.”+