Ekisodo 34:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Mwana woyamba kubadwa wa bulu muzimuwombola ndi nkhosa. Koma ngati simungamuwombole, muzimuthyola khosi. Ndipo muziwombola mwana wanu wamwamuna aliyense woyamba kubadwa.+ Palibe amene ayenera kuonekera kwa ine chimanjamanja.
20 Mwana woyamba kubadwa wa bulu muzimuwombola ndi nkhosa. Koma ngati simungamuwombole, muzimuthyola khosi. Ndipo muziwombola mwana wanu wamwamuna aliyense woyamba kubadwa.+ Palibe amene ayenera kuonekera kwa ine chimanjamanja.