Ekisodo 34:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Zipatso zoyamba kucha zabwino kwambiri zamʼmunda mwanu muzibwera nazo kunyumba ya Yehova Mulungu wanu.+ Musamawiritse mwana wa mbuzi mumkaka wa mayi ake.”+ Ekisodo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 34:26 Nsanja ya Olonda,3/15/2004, tsa. 27
26 Zipatso zoyamba kucha zabwino kwambiri zamʼmunda mwanu muzibwera nazo kunyumba ya Yehova Mulungu wanu.+ Musamawiritse mwana wa mbuzi mumkaka wa mayi ake.”+