Ekisodo 34:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Kenako Aisiraeli onse anamuyandikira, ndipo iye anawapatsa malamulo onse amene Yehova anamupatsa mʼphiri la Sinai.+
32 Kenako Aisiraeli onse anamuyandikira, ndipo iye anawapatsa malamulo onse amene Yehova anamupatsa mʼphiri la Sinai.+