Ekisodo 34:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Koma Mose akamalowa mʼchihema chokumanako kukaonekera kwa Yehova kuti akalankhule naye, ankachotsa chophimbacho mpaka atatulukamo.+ Kenako ankapita kwa Aisiraeli nʼkuwauza zimene walamulidwa.+ Ekisodo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 34:34 Nsanja ya Olonda,7/15/1990, ptsa. 15-16
34 Koma Mose akamalowa mʼchihema chokumanako kukaonekera kwa Yehova kuti akalankhule naye, ankachotsa chophimbacho mpaka atatulukamo.+ Kenako ankapita kwa Aisiraeli nʼkuwauza zimene walamulidwa.+