Ekisodo 35:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 guwa lansembe zopsereza+ ndi sefa wake wa zitsulo zakopa, ndodo zake zonyamulira ndi zipangizo zake zonse komanso beseni ndi choikapo chake.+
16 guwa lansembe zopsereza+ ndi sefa wake wa zitsulo zakopa, ndodo zake zonyamulira ndi zipangizo zake zonse komanso beseni ndi choikapo chake.+