Ekisodo 35:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Apangenso zovala zolukidwa bwino+ zoti azivala potumikira mʼmalo opatulika, zovala zopatulika za Aroni+ wansembe ndi zovala za ana ake zoti azivala potumikira monga ansembe.’”
19 Apangenso zovala zolukidwa bwino+ zoti azivala potumikira mʼmalo opatulika, zovala zopatulika za Aroni+ wansembe ndi zovala za ana ake zoti azivala potumikira monga ansembe.’”