-
Ekisodo 35:24Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
24 Onse amene anapereka chopereka chasiliva ndi kopa anapereka zoperekazo kwa Yehova, ndipo onse amene anali ndi matabwa a mthethe oti akagwire ntchito pa utumiki wonse wapachihema anabwera nawo.
-