Ekisodo 35:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Akazi onse aluso+ anawomba nsalu ndi manja awo, ndipo ankabweretsa zingwe zopota za ulusi wabuluu, ubweya wa nkhosa wapepo, ulusi wofiira kwambiri ndi nsalu zabwino kwambiri.
25 Akazi onse aluso+ anawomba nsalu ndi manja awo, ndipo ankabweretsa zingwe zopota za ulusi wabuluu, ubweya wa nkhosa wapepo, ulusi wofiira kwambiri ndi nsalu zabwino kwambiri.