Ekisodo 36:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Ndipo iwo anatenga kwa Mose zopereka zonse+ zimene Aisiraeli anabweretsa kuti azigwiritse ntchito pa utumiki wopatulika. Koma Aisiraeliwo anapitirizabe kubweretsa kwa Mose nsembe zaufulu mʼmawa uliwonse.
3 Ndipo iwo anatenga kwa Mose zopereka zonse+ zimene Aisiraeli anabweretsa kuti azigwiritse ntchito pa utumiki wopatulika. Koma Aisiraeliwo anapitirizabe kubweretsa kwa Mose nsembe zaufulu mʼmawa uliwonse.