-
Ekisodo 36:6Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
6 Choncho Mose analamula kuti alengeze mumsasa wonsewo, kuti: “Amayi ndi abambo, musabweretsenso zinthu zina kuti chikhale chopereka chopatulika.” Ndi mawu amenewa anthuwo anasiya kubweretsa zinthuzo.
-