Ekisodo 36:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Nsalu iliyonse inali mamita 13* mulitali ndipo mulifupi inali mamita awiri. Nsalu zonse muyezo wake unali wofanana.
9 Nsalu iliyonse inali mamita 13* mulitali ndipo mulifupi inali mamita awiri. Nsalu zonse muyezo wake unali wofanana.