-
Ekisodo 36:11Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
11 Atatero anapanga zingwe zopota zabuluu zokolekamo ngowe mʼmphepete mwa nsalu imodzi pamene nsalu ziwirizo zidzalumikizane. Anachitanso chimodzimodzi mʼmphepete mwa nsalu yakumapeto kwenikweni, pamene nsaluzo zidzalumikizane.
-