-
Ekisodo 36:13Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
13 Pomaliza anapanga ngowe 50 zagolide nʼkulumikiza nsalu za tenti ndi ngowezo moti nsaluzo zinakhala chinsalu chimodzi chopangira chihema.
-