-
Ekisodo 36:17Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
17 Atatero anaika zingwe zopota 50 zokolekamo ngowe mʼmphepete mwa nsalu yakumapeto kwenikweni, polumikizirana nsalu ziwirizi. Anaikanso zingwe zopota 50 zokolekamo ngowe mʼmphepete mwa nsalu inayo, pamalo amene nsalu ziwirizi zinalumikizana.
-