-
Ekisodo 36:22Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
22 Felemu lililonse linali ndi zolumikizira ziwiri zoyandikana. Mafelemu onse a chihema anawapanga choncho.