-
Ekisodo 36:29Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
29 Mafelemu amenewo anali ndi matabwa awiri ophatikiza kuyambira pansi mpaka pamwamba, pamene pali mphete yoyamba. Izi nʼzimene anachita ndi mafelemu onse ochirikiza mʼmakona.
-